MAFUNSO A ANA pA CHIKHULUPILIRO

MAFUNSO A ANA pA CHIKHULUPILIRO

The Children's Questions about Faith

تأليف:

Abd Ar-Rahman bin Abd Alkareem Ash-Sheha

دار النشر : osoulstore
28.75 ر.س Bukuli lagawidwa m’magawo awiri : gawo loyamba (zokhudza maphunziro a chikhulupiliro ), m’menemo muli maziko ambiri omwe angathandize makolo kuphunzitsa ana awo – mu chifuniro cha Allah -, pomwe gawo la chiwiri likuzungulira pa (zitsanzo zochitika pakayankhidwe ka mafunso a ana okhudza chikhululupiliro) m’menemo tiyankhamo mafunso amene ali otchuka kwambiri pakati pa ana amisinkhu yosiyana siyana, makamaka omwe akukhudzana ndi msichi zachikhulupiliro zisanu ndi imodzi (6) ndipo tafotokozamo momveka bwino m’mene tingayankhire mafunso ngati amenewa المزيد من التفاصيل
نبذه عن الكتاب

Bukuli lagawidwa m’magawo awiri : gawo loyamba (zokhudza maphunziro a chikhulupiliro ), m’menemo muli maziko ambiri omwe angathandize makolo kuphunzitsa ana awo – mu chifuniro cha Allah -, pomwe gawo la chiwiri likuzungulira pa (zitsanzo zochitika pakayankhidwe ka mafunso a ana okhudza chikhululupiliro) m’menemo tiyankhamo mafunso amene ali otchuka kwambiri pakati pa ana amisinkhu yosiyana siyana, makamaka omwe akukhudzana ndi msichi zachikhulupiliro zisanu ndi imodzi (6) ndipo tafotokozamo momveka bwino m’mene tingayankhire mafunso ngati amenewa

تفاصيل الكتاب
  • ردمك (ISBN):9786038352304
  • تأليف:Abd Ar-Rahman bin Abd Alkareem Ash-Sheha
  • دار النشر:osoulstore
  • التصنيف:الكتب الإسلامية والدينية
  • اللغة:السواحلية
  • سنة النشر:2022
  • عدد الصفحات:152
  • الغلاف:تغليف ورقي
  • الوزن (كجم):0.35
ردمك (ISBN)9786038352304
دار النشرosoulstore
التصنيفالكتب الإسلامية والدينية
اللغةالسواحلية
سنة النشر2022
عدد الصفحات152
الغلافتغليف ورقي
الوزن (كجم)0.35

كتب ذات صلة

50.00 ر.س
26.00 ر.س

كتب لنفس البائع

22.00 ر.س